23Moyo uposa chakudya, ndi thupi liposa chovala.
24Taonani makwangwala: iwo safesa kapena kukolola, alibe nyumba zosungamo zinthu kapena nkhokwe; komabe, Mulungu amawadyetsa. Koposa kotani inu amene ndi ofunikira kuposa mbalame.
25Ndi ndani wa inu akhoza kuwonjeza ora pa moyo wake chifukwa cha kudandaula?