Pular para o conteúdo
Publicidade

YESAYA 43

6 Ndidzawuza a kumpoto kuti, Amasuleni,

ndidzawuza akummwera kuti, Musawagwire.

Bweretsani ana anga aamuna kuchokera ku mayiko akutali,

ana anga a akazi kuchokera kumalekezero a dziko lapansi;

7 onsewo amadziwika ndi dzina langa;

ndinawalenga chifukwa cha ulemerero wanga,

ndinawawumba, inde ndinawapanga."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também