Pular para o conteúdo
Publicidade

YESAYA 45

9 "Tsoka kwa wokangana ndi mlengi wake,

ngakhale kuti ali ngati phale chabe pakati pa mapale anzake.

Kodi dongo lingafunse munthu wowumba kuti,

Kodi ukuwumba chiyani?

Kodi ntchito yako inganene kuti,

Ulibe luso?

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também