Pular para o conteúdo
Publicidade

YESAYA 6

9 Yehova anati, "Pita ndipo ukawawuze anthu awa:

" Kumva muzimva, koma osamvetsetsa;

kupenya muzipenya koma osaona kanthu.

10 Tsono anthu amenewa uwaphe mtima;

uwagonthetse makutu,

ndipo uwatseke mʼmaso.

Mwina angaone ndi maso awo,

angamve ndi makutu awo,

angamvetse ndi mitima yawo,

kenaka ndi kutembenuka mtima ndi kuchiritsidwa."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também