14 Yachiteni yonjhe popande kudandaula wala kulimbana, 15 ili mkhale wana wa Mnungu mulibe lawama ni hatiya, ata ngati mukhala nikuzungulilidwa niwandhu anyiyawo akhala mujhiko loyipa ni lotayika simung’azikile pakati pao ngati umo ndhondwa zing’azila pajhiko,