20 Nambho, kukhomo kwatu kumwamba, nafe timlindilila kwa khumbilo Kilisito kuchokela kumwamba, mate yake Ambuye Yesu Kilisito. 21 Yawo siang’anamule mathupi yathu ya kumwalila ili tipate thupi lake losa mwalile kwa kukhoza kujha wakhoza kuviika vindhu vonjhe paulamulo wake.