Pular para o conteúdo
Publicidade

Aloma 10:13-17

NTNYBL2025 Nyanja

13 Yalembedwa chimwechi mmalembo ya Mnungu, "Mundhu waliyonjhe uyo siwapembhe kwa ulamuli wa jhina la Ambuye siwaomboledwe."

14 Chipano sampembhe bwanji iye samkhulupilila? Nianyiiwo, samkhulupilile bwanji ngati sadavela nghani zake? Nisavele bwanji ngati palibe mundhu olalikila? 15 Ni wandhu salalikile bwanji ngati sadapelekedwe? Ngati umo yalembedwa mmalembo ya Mnungu, "Chindhu chokwada kupunda kujha kwa wajha alalikila Uthenga Wabwino!" 16 Nambho asati wonjhe adaulandila Uthenga Wabwino. Nde ndande Isaya wadakamba, "Mbuye ni yani uyo wadakhulupilila uthenga wathu?" 17 Chimwecho, chikhulupi chichokana ni kuvela Uthenga Wabwino, ni uthenga umeneo uchokana ni mawu la Kilisito.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    13 pakuti, "Aliyense amene adzayitana pa dzina la Ambuye adzapulumuka."

    14 Kodi adzayitana bwanji amene sanamukhulupirire? Ndipo adzakhulupirira bwanji asanamve za Iye? Ndipo adzamva bwanji popanda wina kulalikira kwa iwo? 15 Ndipo iwo adzalalikira bwanji osatumidwa? Kwalembedwa kuti, "Akongoladi mapazi a iwo amene amabweretsa Uthenga Wabwino!"

    16 Koma si onse amene anavomereza Uthenga Wabwino. Pakuti Yesaya akuti, "Ambuye, ndani amene wakhulupirira uthenga wathu?" 17 Motero, chikhulupiriro chimabwera pamene timva uthenga ndipo uthenga umamveka kuchokera ku mawu a Khristu.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.