1 Tikambe chiyani chipano? Bwanji tiendekele kukhala mmachimo kuti ubwino wa Mnungu uchuluke? 2 Notho! Ife tayafela machimo, sitiendekele bwanji kukhala mmachimo? 3 Mjhiwa ife tidabatizidwa tidalunjana ni Yesu Kilisito, tidabatizidwa ni kulunjana ni nyifa yake. 4 Yapo tidabatizidwa tidalunjana ni nyifa yake, tidazikidwa pamojhi niiye, kuti ngati mujha kilisito wadahyukichidwa kwa mbhavu yaikulu ya Atate, ife nafe tikhoze kukhala ni umoyo wa chipano.
5 Pakuti ife talunjana niiye kwa njila nyifa yake, chimwecho ife sitilunjane naye kwa kuhyukichidwa ngati iye. 6 Tijhiwa kuti vichito vathu va kale vidafa ni vidapachikidwa pa mtanda pamojhi niiye, kuti mbhavu za machimo ziwanangidwe, ni sitidakhalanjho akapolo a machimo. 7 Mundhu wakafa kwa mtundu umeneo siwakhaliletu hulu kuchokela mmbhavu za machimo. 8 Chipano, tamwalila pamojhi ni Kilisito, tikhulupilila kuti sitikhale pamojhi niiye. 9 Chipano tijhiwa Kilisito watohyukichidwa siwamwalilanjho ni nyifa simlamulanjho. 10 Chimwecho pakuti wadamwalila mala kamojhipe ni wadaikoza mbhavu ya machimo, sazino ni wamoyo ni paumoyo wake wamkwadilicha Mnungu, 11 Chinchijha anyiimwe ifunika mjhione kuti mwafa kwa nghani ya machimo, nambho ngati mkhala kwa umojhi ni Mnungu kwa kumkhulupilila Yesu Kilisito.
12 Chipano machimo siyadalamulanjho wiwalo va matupi yanu yayo siyafe, ni siyadakuchitani muyavele makumbilo yanu. 13 Msidachichita chiwalo chilichonjhe cha matupi yanu kuhala chindhu cho chitila machimo. Pambuyo pake jhichocheni mwachinawenewake kwa Mnungu ngati wandhu mwa hyuka, vichocheni viwalo vanu kwa Mnungu ngati vindhu ivo vavomelezeka. 14 Machimo siyakulamulilani njhoni, pakuti anyiimwe simchogozedwa ni thauko, nambho mchogozedwa ni ubwino.
15 Chipano tikambe chiyani? Tichite machimo ndande sitichogozedwa ni thauko nambho tichochogozwedwa ni ubwino? Notho! 16 Mjhiwa kuti anyiiwe mkajhichocha mwachina wene ngati akapolo wa mundhu waliyonjhe mkhala akapolo azene amundhu yujha, ni ngati mkachichocha kukhla akapolo wa machimo mathelo yake ni nyifa, nambho mkachichocha kumvela Mnungu simkhale ovemelezeka kwa Mnungu? 17 Nambho chipano nimuyamika Mnungu, pakuti anyiimwe kale mdali akapolo amachimo, mwakhala ovela kwa mtima yanu yonjhe kwa mayaluzo mdayaluzidwa. 18 Mdaomboledwa kuchokela kuukapolo wa machimo, chipano mwakhala akapolo akuchita yajha yamkwadilicha Mnungu. 19 Nakamba ni anyiiimwe kwa kutumia mkambo uno wa akapolo kuti mkoze kujhiwa icho nakamba, kale mdali akapolo a machimo kwa kujhichocha mwachinawene kukhala vindhu vochita vindhu voipa ni machimo yanu yadali yambili kupunda, nambho saino ifunika mjhichoche kwa mnungu pa umoyo wanu wonjhe. Mkhale akapolo kwa vindhu ivo vimkwadilicha Mnungu. Mjhichita vindhu vavomelezeka ni Mnungu mwene kulangiza kuti anyiimwe ni wandhu wa Amnungu.
20 Kale mdali akapolo amachimo, simdaganizile kuchita vindhu ivo vimkwadilicha Mnungu. 21 Chipano mdapata chiyani siku zijha kuchokana ni vindhu vijha mvionela njhoni saino? Pakuti vindhu ivi vipeleka nyifa! 22 Nambho saino mwalekeleledwa kuchokela ku ukapolo wa machimo, ni mwakhala akapolo a Mnungu, mwakhala wandhu wake ni mathelo yake simpate umoyo wa muyaya. 23 Pakuti ukayatumikila machimo siufe, nambho mbhaso iyo wachocha Mnungu ni umoyo wa muyaya kwa kulunjana ni Kilisito Yesu, Ambuye wathu.