Pular para o conteúdo
Publicidade

Aloma 10:8,9

NTNYBL2025 Nyanja

8 Malembo ya Mnungu yakamba chimwechi, "Uthenga umeneo wa Mnungu uli pafupi ni iwe, uli mkamwa mwako ni mumtima mwako" Nayo nde chijha chikhulupi tilalikila. 9 Ngati ukakamba kwa pakamwa pako kuti Yesu ni Mbuye, ni kukhulupilila mumtima mwako kuti Mnungu wadamuhyukicha, siuomboke.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    8 Nanga akuti chiyani? "Mawu ali pafupi ndi inu. Ali mʼkamwa mwanu ndi mu mtima mwanu." Ndiwo mawu achikhulupiriro amene ife tikuwalalikira, 9 kuti ngati udzavomereza ndi pakamwa pako kuti, "Yesu ndiye Ambuye," ndi kukhulupirira mu mtima mwako kuti Mulungu anamuukitsa kwa akufa, udzapulumuka.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.