Pular para o conteúdo
Publicidade

Aloma 12:1,11

NTNYBL2025 Nyanja

Ukhalo wa kumtumikila Mnungu

1 Chipano, achabale wanga, pakuti Mnungu ni walisungu kupunda, nikupembhani kwa mtima wanga wonjhe, mjhichoche mwachinawene kwa Amnungu mkhale ngati njhembe yo pyeleza iyo ili yamoyo, iyo ili ya Mnungu mwene ni yomkwadilicha Mnungu. Iyi nde njila yanu ya zene yakumlambila Mnungu.

11 Msidakhala alesi kuchita jhito ya Mnungu, mchite njhito imeneyo kwa mtima onjhe ni kumtumikila Mnungu.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    1 Nʼchifukwa chake ine ndikukupemphani abale, mwa chifundo cha Mulungu, kuti mupereke matupi anu monga nsembe yamoyo, yopatulika ndi yokondweretsa Mulungu. Nsembeyi ndiye kupembedza kwanu kwa uzimu.

    11 Musakhale aulesi mʼmachitidwe anu. Khalani achangu mu mzimu ndipo tumikirani Ambuye.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.