Pular para o conteúdo
Publicidade

Aloma 4:6,7

NTNYBL2025 Nyanja

6 Naye Daudi wakambanjho chimwecho ndande ya kukondwa uko walinako mundhu uyo wavomelezedwa ni Mnungu kuti ni woyela, popande kukhulupilila vichito vake,

7 "Sakondwele wandhu yawo alekeleledwa machimo yao,

yawo machimo yao vafutidwa.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    6 Davide ponena zomwezi pamene anayankhula za kudala kwa munthu amene Mulungu amulungamitsa osati chifukwa cha ntchito zake akuti,

    7 "Odala ndi amene

    zoyipa zawo zakhululukidwa;

    amene machimo awo afafanizidwa.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.