20 Thauko yapo lidachokela, lidapelekela kuchuluka kwa voipa, nambho machimo yapo yadachuluka, ubwino udapunda kuchuluka. 21 Ngati umo machimo umo yadali ni mbhavu ya kwapelekela wandhu, chimchijha ubwino wachita wandhu avomelezeke ni Mnungu kwa kwapeleka umoyo wa muyaya kwa njila ya Yesu kilisito, Mbuye wathu.
Publicidade
Aloma 5:20,21
NTNYBL2025 Nyanja
Em outras traduções
- TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo
20 Malamulo a Mulungu anaperekedwa ndi cholinga chakuti anthu onse azindikire kuchuluka kwa machimo awo. Koma pamene machimo anachuluka, chisomo chinachuluka koposa. 21 Choncho monga momwe tchimo linkalamulira anthu ndi kubweretsa imfa pa iwo, chomwecho kunali koyenera kuti chisomo chilamulire pobweretsa chilungamo kwa anthu, ndi kuwafikitsa ku moyo wosatha mwa Yesu Khristu Ambuye athu.
Direitos das traduções citadas
Estes versículos te tocaram? Ore agora!
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.