8 Nambho Mnungu wachimikiza kuti watikonda, pakuti yapo tidali tikali amachimo, kilisito wadafa ndande yathu. 9 Pakuti saino tavomelezeka ni Mnungu kwa mwazi wa kilisito, chimwecho sitiomboledwe kuchokela mmbwayi yaikulu ya Mnungu!
Publicidade
Aloma 5:8,9
NTNYBL2025 Nyanja
Em outras traduções
- TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo
8 Koma Mulungu anaonetsa chikondi chake kwa ife chifukwa pamene tinali ochimwabe, Khristu anatifera.
9 Popeza chifukwa cha magazi ake ife tapezeka olungama pamaso pa Mulungu, Iyeyo adzatipulumutsa koposa kotani ku mkwiyo wa Mulungu.
Direitos das traduções citadas
Estes versículos te tocaram? Ore agora!
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.