5 Pakuti anyiwajha akhala kwa kulichata thupi, achogozedwa ni maganizo ya thupi, nambho anyiwajha akala ngati ufunila mzimu wa Mnungu, achogozedwa ni maganizo ya mzimu. 6 Maganizo yayo yachogozedwa ni thupi yapeleka nyifa, nambho maganizo yayo yachogozedwa ni Mzimu yapeleka umoyo ni mtendele.
Publicidade
Aloma 8:5,6
NTNYBL2025 Nyanja
Em outras traduções
- TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo
5 Pakuti anthu amene amakhala monga mwa makhalidwe oyipa a thupi amayika malingaliro awo pa zinthu zathupi. Koma amene amakhala monga mwa Mzimu amayika malingaliro awo pa zinthu za Mzimu. 6 Kuyika mtima pa zathupi ndi imfa koma kuyika mtima pa za Mzimu ndi moyo ndi mtendere.
Direitos das traduções citadas
Estes versículos te tocaram? Ore agora!
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.