5 jhiko likali losaumbidwe Mnungu kutisangha, tikhale wana wake kupitila Yesu Kilisito nde umo wadakondela ni chifuno chake mwene.
6 Chimwecho, timtamande Mnungu kwa ulemelelo wa ubwino wake uwo watipacha ife kwakupitila mwana wake wa payokha.