Pular para o conteúdo
Publicidade

Gálatas 1

Uthenga wabwino ni umojhipe

6 Nizizwa kupunda ndande yandopitape ndhawi yochepa anyiimwe mwamsiya Mnungu uyo wadakutanani kwa ubwino wa Kilisito, anyiimwe mchata Uthenga wabwino wina uwo uoneka ngati Uthenga Wabwino. 7 Zenedi asati Uthenga Wabwino. Uzene ni kuti alipo wandhu yawo akusakalichani, wandhu yao afuna kuyapundula mayaluzo ya Kilisito. 8 Nambho ata ngati mmojhi wanu kapina mtumiki wa kumwamba wa Amnungu wakakulalikilani Uthenga wina uwo uoneneka ngati Uthenga Wabwino kusiyana ni ujha tidakulalikilani, walesedwe mundhu mmeneyo! 9 Ngati mujha tidakukambilani, ni saino nikambanjho, ngati mundhu waliyonjhe wakakulalikilani Uthenga wina kusiyana ni ujha mdalikidwa, walesedwe mundhu mmeneyo!

Veja também

Gálatas
Ver todos os capítulos de Gálatas