Pular para o conteúdo
Publicidade

Aloma 11:33-36

NTNYBL2025 Nyanja

Mnungu watamandidwe

33 Yetu, Mnungu wali ni chuma chambili kupunda, kujhiwa ni njelu ya Mnungu vilibe mathelo! Lisungu lake silipenyeka, ni njila zake sizijhiwaka!

34 Ngati umo yalembedwa, "Yani uyo wayajhiwa maganizo ya Ambuye?

Yani wakhoza kukhala mundhu wa kumthangatila maganizo?

35 Yani uyo wampacha Mnungu chindhu chalichonjhe

kuti wakhoze kubwezeledwa chindhu chimenecho?" 36 Pakuti vindhu vonjhe vichokela kwake, ndande yake vonjhe viendekela kukhalapo. Ulemelelo ukhale kwake ni hadi muyaya ikhale chimwecho.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    33 Aa! Nzeru za Mulungu ndi chidziwitso chake ndi zozama kwambiri!

    Ndani angazindikire maweruzidwe ake,

    ndipo njira zake angazitulukire ndani?

    34 "Kodi wadziwa ndani maganizo a Ambuye?

    Kapena ndani anakhalapo mlangizi wake?"

    35 "Kodi ndani anapereka mphatso kwa Mulungu,

    kuti Mulunguyo amubwezere iye?"

    36 Pakuti zinthu zonse nʼzochokera kwa Iye, nʼzolengedwa ndi Iye ndipo zimabweretsa ulemerero kwa Iye.

    Kwa Iye kukhale ulemerero mpaka muyaya! Ameni.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.