17 Ngati umo yalembedwela mmalembo ya Mnungu, "Nakuika ukhale tate wa wandhu a maiko yambili." Mawu yameneyo ni ya uzene pachogolo pa Mnungu uyo wadamkhulupilila Ibulahimu, Mnungu uyo waapacha wandhu akufa umoyo, ni kwa lamulo lake vindhu ivo sividakhalepo vikhalapo. 18 Ibulahimu pajha wadakambidwa mawu yajha yadali yolimba kuyakhulupila, nambho Ibulahimu wadaendekela kukhulupilila kuti Mnugnu siwamchite kukhala tate wa wandhu a maiko yambili, ngati umo yalembedwa mmalembo, "Mibadwa yako siikhale yambili ngati ndhondwa!" 19 Wadali mzee, ni vyaka vake vidawandikila miya mojha nambho pamojhi ni chimenecho chikhulupililo chake sichidachepekele ata ngati wadajhiwa kuti siwakhozanjho kupata mwana thupi lake lidali ngati lafa ni mkazake sala wadali wambende. 20 Ibulahimu siwadakhaikile lijha lidakambidwa ni Mnungu, wadapata mbhavu kuchokana ni chikhulupililo, wadayendekela kumkhulupilila ni kumpacha ulemelelo. 21 Ibulahimu wadajhiwa zenedi kuti Mnungu wakhoza kuyakwanilicha yajha wadakamba kuti siwatipache.
Aloma 4:17-21
Em outras traduções
- TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo
17 Monga kwalembedwa kuti, "Ine ndakusandutsa kukhala kholo la mitundu yambiri." Iye ndiye kholo lathu pamaso pa Mulungu, amene anamukhulupirira, Mulungu amene amapereka moyo kwa akufa ndipo amapereka moyo kwa zinthu zopanda moyo.
18 Ngakhale zinali zosayembekezeka, Abrahamu anakhulupirira ndi chiyembekezo kuti adzakhala kholo la mitundu yambiri. Izi ndi monga zinanenedwa kwa iye kuti, "Ndi mmene adzakhalire ana ako ndi zidzukulu zako." 19 Iye sanafowoke mʼchikhulupiriro. Anadziwa choonadi cha thupi lake kuti linali lakufa popeza anali ndi zaka pafupifupi 100 ndiponso mimba ya Sara inali yowuma. 20 Komabe iye sanagwedezeke chifukwa chosakhulupirira pa zokhudzana ndi lonjezo la Mulungu. Iye analimbikitsidwa mʼchikhulupiriro chake ndi kupereka ulemerero kwa Mulungu. 21 Anatsimikiza mu mtima mwake kuti Mulungu anali ndi mphamvu yochita chomwe analonjeza.
Direitos das traduções citadas
Estes versículos te tocaram? Ore agora!
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.