Pular para o conteúdo
Publicidade

Aloma 5:1-4

NTNYBL2025 Nyanja

Mate ya kuvomelezeka ni Mnungu

1 Pakuti Mnungu watichita kukhala oyela kwa kumkhulupilila iye, chipano tili ni mtendele nawo, kwa njila ya Yesu Kilisito. 2 Kwa kumkhulupilila Yesu, iye watipacha ubwino wake. Mbaka chipano tiendekela kukhala mu ubwino umeneo. Chipano tikondwela kupunda ndande ya chikhulupi chathu sitikhale pamojhi muulemelelo wa Mnungu. 3 Osati yameneyope nambho tikondwela mavuto uku ni tijhiwa kuti mavuto yapeleka kulimba mtima pa kumkhulupilila Yesu, 4 ni kulimba mtima pa kumkhulupilila Yesu kupeleka kuchimikiza kwa mtima ni kuchimikiza kwa mtima kupeleka kukhulupilila.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    1 Tsopano popeza tayesedwa olungama mwa chikhulupiriro, tili ndi mtendere ndi Mulungu kudzera mwa Ambuye athu Yesu Khristu. 2 Iyeyo ndiye amene anatsekulira njira mwachikhulupiriro yolowera mʼchisomo mʼmene takhazikikamo. Ndipo tikukondwerera chiyembekezo cha ulemerero wa Mulungu. 3 Koma si pokhapo ayi, koma ife tikukondweranso mʼmasautso athu chifukwa tikudziwa kuti masautso amatiphunzitsa kupirira. 4 Ndipo kupirira kumabweretsa makhalidwe, makhalidwe amabweretsa chiyembekezo.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.