18Chimwecho ni onjhe anyiyao amwalila uku amkhulupila Kilisito atayika.
26Nyifa nde mdani wothela uyo siwayomwechedwe.
30Niife ndande yanji tali muhatali ndhawi zonjhe?
27 resultados encontrados
18Chimwecho ni onjhe anyiyao amwalila uku amkhulupila Kilisito atayika.
26Nyifa nde mdani wothela uyo siwayomwechedwe.
30Niife ndande yanji tali muhatali ndhawi zonjhe?
1Nikonda kumjhiwicha kwanu mlongo wathu Foibe, uyo wali mtumiki pa gulu la wandhu amkhulupilila Yesu ku Kenikelea.
5Walonjele wandhu amkhulupilila Yesu yawo apezana kukhomo kwako.Moni zanga zimfikile mbwenji wanga Epaineto uyo wadali woyamba ku mkhulupilila Yesu ku jhiko la Asia
24Ubwino wa Ambuye watu Yesu Kilisito ukhale pamojhi nianyiimwe. Ikhale chimwecho.
4ni wonjhe adamwa chakumwa chinchijha chidacho kwa Mnungu. Adamwa kuchoka mujha mumwala waukulu wa uzimu uwo udachata, ni mwala waukulu umeneo udali Kilisito mwene wake.
24Mundhu, waliyonjhe siwada funafuna vindhu vake mwene nambho wafunefune ni vindhu va wina.
26Kwaife, yalembedwa mu malembo ya Mnungu, "Jhiko ni vindhu vonjhe ivo vilimo ni chuma cha Mbuye."
12Chipano kwa kulunjana ni Kilisito ni kumkhulupilila, tipilila kumuwandikila Mnungu kwa kumkhulupilila.
15uyowali chiyambo cha voumbidwa vonjhe va kumwamba ni pajhiko.
17dala Kilisito wakhale mkati mwanu kwa njila ya kumkhulupilila. Nimpembha Mnungu yonjhe yayo muyachita yachoke muchikondi cha zene,
8Kale anyiimwe mdali mumdima simmamjhiwe Mnungu, nambho chipano muli mudangalila, mumjhiwa Mnungu kwa kulunjana ni Ambuye Yesu. Mkhale umo wafunila Mnungu,
14ndande chilichonjhe icho chavumbulidwa, chikhala dangalila. Nde ndande yalembedwa Mumalembo ya Mnungu,"Uka iwe waghona,uhyuke,Kilisito siwakuwalichile dangalila lake."
30pakuti ife ni viwalo va thupi lake.
14Wonjhe achogozedwa ni Mzimu wa Mnungu ni wana wa Amnungu.
24Pakuti kwa kukhulupila kumeko ife taomboledwa. Nambho kukhulupilila kulibe mate ngati tichiona chijha tichikhulupilila. Pakuti yani wakhulupilila chijha wachiona?
25Ngati tichikhulupila icho tilibe, chimwecho sitichilindile kwa kuchilimbila mtima.
1Yesu waadakambila, "Simudadandaula mumitima yanu. Mwaakhulupilila Amnungu, munikhulupilile ni ine.
17Iye ni Mzimu wa zene. Jhiko lapanjhi silikhoza kumlandila ndande silimuona kapina kumjhiwa. Nambho anyiimwe mumjhiwa ndande wakhala namwe ni wali mkati mwanu."
29Chipano nakukambilani yakali yosa chokele, ndande yapo siyachokele mukhulupilile.
3Uzene ni kuti anyiimwe nde kalata yalembedwa ni Kilisito iyo yapelekedwa kupitila ife. Siidalembedwe kwa wino, nambho yalembedwa kwa Mzimu wa Mnungu uyo wali wa Moyo, siidalembedwe pa chibandhu cha mwala, nambho yalembedwa mmitima mwanu.
8utumiki wa Mzimu wa Mnungu ukhala ni ulemelelo waukulu kupunda.
12Tili ni kulimba mtima kupunda pakuti tili ni chikhulupililo cha mtundu uwu.
47Nikukambilani zene, uyo wakhulupilila wali ni umoyo wa muyaya.
48Ine nde chakudya cha umoyo.
69Ife tikhulupilila, ni tijhiwa kuti imwe nde yujha Oyela Amnungu"
17Poolo yapo wadali ku Mileto, wadatuma uthenga kupita ku Efeso, kwaatana azee awandhu yawo adamkhulupilila Kilisito kuti akomane naye.
21Nidamkambila wandhu wonjhe, Ayahudi ni osati Ayahudi, kuti alape ni amng’anamukile Mnungu, ni mwakhulupilile Ambuye wathu Yesu.
28Chipano, jhipenyeleleni anyiimwe pamojhi ni wandhu wonjhe yawo mwapachidwa ni Mzimu Woyela. Asungeni wandhu amkhulupilila Yesu yawo Amnungu waagula kwa mwazi wa mwana wao.
23Nyengo imeneyo kudachokela mkangano waukulu ku Efeso ndande ya nghani ya Ambuye.
26Nambho penyani icho wachita mundhu uyu. Iye wakamba kuti minungu iyo yakonjedwa ni wandhu osati minungu ya zene ata pang’ono. Iye wadyelekezela wandhu ambili mu Efeso ni Asiya kulambila minungu yawo.
35Pambuyo pa ndhawi, mchogoleli mmojhi wa mujhi ujha wadaakhalicha chete wandhu. Iye wadakamba, "Anyiimwe wandhu aku Efeso, bwanji, simjhiwa kuti wandhu a mmujhi wa Efeso nde yawo alonda nyumba ya nungu Atene uyo wali wamkulu, ni mwala wake udagwa kuchokela kumwamba?
3Mundhu waliyonjhe wakajhiona kuti iye ni wamate, nikumbe osati wamate wajhinyenga mwene.
7Simdanyengeka, Amnungu sachitidwa chipongwe. Icho wavyala mundhu nde icho siwakolole
18Abale wanga, mwawi wa Ambuye wathu Yesu Kilisito ukhale nianyiime. Ikhale chimwecho.
3"Vechelani! Wovyala wadapita kumijha mbewu.
12kuti,‘Apenye, nambho siadaona.Avele, nambho sazindikila.Adakajhiwa, adakambwelela Mnungu,Nayo wadakalekelela machimo yao.’"
14Wovyala wavyala Mawu la Mnungu.
4Chimwemwe chanu mwa Ambuye kwambili. Nikamba muchimwemwe!
5Upole wanu ujhiwike ni wandhu onjhe. Ambuye ali pafupi.
9Vindhu vonjhe mwajiyaluza kwanga kapina kuyalandila kapina kuyavela kapina kuyaona, yachiteni yameneyo. Ni Mnungu watupacha mtendele siwakhale pamojhi nianyiimwe.
41Yesu wadayangha, "Anyiimwe ni mbadwa woipa ni wopande chikhulupililo, sinikhale na anyiimwe kwa ndhawi yaitali yanji kuti munikhulupilile?" Ndiipo Yesu wadamkambila mudhu yujha, "Majhanayo mwana wako pano."
55Nambho Yesu wadang’anamukila ni kwakaniza.
56Yesu pamojhi ni oyaluzidwa wake adachoka ni kupita kumujhi wina.
3Osati yameneyope nambho tikondwela mavuto uku ni tijhiwa kuti mavuto yapeleka kulimba mtima pa kumkhulupilila Yesu,
4ni kulimba mtima pa kumkhulupilila Yesu kupeleka kuchimikiza kwa mtima ni kuchimikiza kwa mtima kupeleka kukhulupilila.
15Nambho kulakwa kwa Adamu sikukhoza kulinganichidwa ni ubwino wa Mnungu. Mate ingakale machimo ya Mundhu Mmojhi yadapeleka nyifa kwa wonjhe. Kwa mundhu mmojhi, yaani Adamu, idakhala ndande ya nyifa kwa wandhu ambili kuchokana ni machimo yake. Nambho kwa ubwino wa mundhu mmojhi, mate yake Yesu, iye waapacha wandhu ubwino wa kuomboledwa machimo yawo.
10Zene Mnungu siwakamba yaya ndande yathu? Zene yalembedwa ndande yathu, pakuti mlimi wa vakudya wavomeleka kulima kwa chikhulupi, ni iye okolola vakudya wadikila kupheza vakudya.
18Chimwecho mkokolo wanga chindhu chanji, basi? Mkokolo wanga ni kulalikila Uthenga Wabwino chajhe, popande kufuna mkokolo wa kulalikila Uthenga Wabwino.
24Zene mujhiwa kuti paliwilo onjhe atamanga, nambho ni mmojhipe nde uyo wapachidwa mbhaso. Chimwecho tamangani liwilo dala mpate mbhaso.
2Kuyambila mmayambo Mawu wadali ni Amnungu.
9Ili nde lidali dangalila la zene, dangalila ilo likujha pajhiko ni kwawalila wandhu wonjhe.
24Wandhu anyamenewo adatumidwa ni Afalisayo.
6wamayesanjho kuchita vindhu ivo sivifunika pa Nyumba ya Mnungu, nambho tidamkaniza. Timafuna kumlamula kwa umo likambila lamulo lathu.
14Icho ine nivomela ni ichi, ine nimlambila Mnungu wa achaatate wathu, ni kukhala kuchatana ni njila iyo anyiyawa Ayahudi aitana kuti njila ya mayaluzo ya mthila. Nambho nikhulupililanjho mu kila chindhu icho chalembedwa ni Thauko ni chijha icho chalembedwa mu vikalakala va alosi.
16Chimwecho masiku yonjhe niyesa kukhala ni mtima wa bwino pachogolo pa Mnungu ni wandhu wonjhe."
13Mnungu wa chikhulupi uyo wakuthilani anyiimwe mtima ni mtendele pa kumkhulupilila, mpate kujhazidwa ni chikhululupilo chachikulu kwa mbhavu za mzimu wa Mnungu.
16ubwino wa ine kukhala mtumiki wa Yesu Kilisito kwa wandhu a maiko yina. Ni njhito yanga ya chijhukulu, kuuzila Uthenga Wabwino wa Mnungu dala wandhu amaiko yina akhoze kukhala njhembe yopyeleza iyo ivomelezeka ni Mnungu, njhembe iyo yaelechedwa ni Mzimu wa Mnungu.
33Mnungu uyo wapeleka mtendele wakhale pamojhi ni anyiimwe mwawonjhe! Ikhale chimwecho!