15 Nambho ngati tikauchota uzene kwa mtima wa chikondi sitikule chizimu ni sitimfikile Kilisito pa vindhu vonjhe, iye nde mlamuli wathu. 16 Kwa kuchogozedwa ni Kilisito, thupi lonjhe likalunjidwa ni kugwilizidwa pamojhi, kwa mthandizo wa kila chiwalo. Chipano, kila chiwalo chichita njhito yake, thupi lonjhe likula lene ni kujhikonja muchikondi.