Pular para o conteúdo
Publicidade

2 Coríntios 11:13-15

NTNYBL2025 Nyanja

13 Achameneo atumwi amthila, anyiyao anyenga njhito zao, yao niajhichita achinawene kuti atumwi auzene a Kilisito. 14 Simdadabwa, pakuti ata satana mwene wadajhichita mtumiki wa dandangalila wa kumwamba. 15 Chimwecho siidabwicha, pakuti ata atumiki asatana ajhichita kuti atumiki abwino pachogolo pa Mnungu. Pothela sapate icho afunikila kuchipata kuchatana ni vichito vao.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    13 Pakuti anthu oterewa ndi atumwi onama, antchito achinyengo, odzizimbayitsa ngati atumwi a Khristu. 14 Sizododometsa zimenezi, pakuti Satana mwini amadzizimbayitsa kuoneka ngati mngelo wowunikira anthu. 15 Nʼzosadabwitsa tsono ngati atumiki ake akudzizimbayitsa ngati otumikira chilungamo. Matsiriziro awo adzalandira zoyenerana ndi ntchito zawo.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.