Pular para o conteúdo
Publicidade

2 Coríntios 11:26

NTNYBL2025 Nyanja

26 Mmaulendo mala zambili nazengedwa ni mafuliko ya majhi, nidavutika kwa kubulidwa ni anghungu, nidavutika kuchokela kwa wandhu ajhiko langa, nidavutika kuchokela kwa wandhu amaiko ina, nidavutika mmijhini, nidavutika mmatengo, nidavutika mnyanja nchele, nidavutika kuchokela kwa achabale aunami.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    26 Ndakhala ndikuyenda maulendo ataliatali. Moyo wanga wakhala ukukumana ndi zoopsa pa mitsinje, zoopsa za achifwamba, zoopsa zochokera kwa abale anga Ayuda, zoopsa zochokera kwa anthu akunja. Ndinakumana ndi zoopsa mʼmizinda, mʼmidzi, pa nyanja, ndi pakati pa abale onyenga.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.