11Chipano, achabale, nikulailani! Mkhale okwanila, gwilani mayaluzo yanga, mkhale chindhu chimojhi, mkhale kwa mtendele. Mnungu wa chikondi ni mtendele siwakhale pamojhi namwe.
12Pajha mpezana mlonjelane kwa chikondi cha chikondi.
13Wandhu wonjhe a Mnungu kumeneko akulonjelani.