Pular para o conteúdo
Publicidade

Aloma 12

19 Okondedwa wanga, simdabwelezela mbwezo, nambho msiileni Mnungu chindhu chimenecho, pakuti yalembedwa mmalembo ya Mnungu, "Nghani ya kubwezela mbwezo ni njhito yanga, ine sinibwezele Ambuye akamba." 20 Yalembedwa malembo yanjake kuti, "Mdani wako wakakhala ni njala mpache chakudya, wakakhala ni lujho mpache majhi. Pakuti kwa kuchita chimwecho simwachite alenge njhoni kupunda." 21 Siudavomela kulepela ni voipa, nambho ukukhoze kuipa kwa ubwino.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também