1 Pakuti Mnungu watichita kukhala oyela kwa kumkhulupilila iye, chipano tili ni mtendele nawo, kwa njila ya Yesu Kilisito. 2 Kwa kumkhulupilila Yesu, iye watipacha ubwino wake. Mbaka chipano tiendekela kukhala mu ubwino umeneo. Chipano tikondwela kupunda ndande ya chikhulupi chathu sitikhale pamojhi muulemelelo wa Mnungu.
Publicidade
Publicidade