Pular para o conteúdo
Publicidade

Romanos 6

2 Notho! Ife tayafela machimo, sitiendekele bwanji kukhala mmachimo? 3 Mjhiwa ife tidabatizidwa tidalunjana ni Yesu Kilisito, tidabatizidwa ni kulunjana ni nyifa yake. 4 Yapo tidabatizidwa tidalunjana ni nyifa yake, tidazikidwa pamojhi niiye, kuti ngati mujha kilisito wadahyukichidwa kwa mbhavu yaikulu ya Atate, ife nafe tikhoze kukhala ni umoyo wa chipano.

5 Pakuti ife talunjana niiye kwa njila nyifa yake, chimwecho ife sitilunjane naye kwa kuhyukichidwa ngati iye. 6 Tijhiwa kuti vichito vathu va kale vidafa ni vidapachikidwa pa mtanda pamojhi niiye, kuti mbhavu za machimo ziwanangidwe, ni sitidakhalanjho akapolo a machimo. 7 Mundhu wakafa kwa mtundu umeneo siwakhaliletu hulu kuchokela mmbhavu za machimo.

Veja também