24 Pakuti kwa kukhulupila kumeko ife taomboledwa. Nambho kukhulupilila kulibe mate ngati tichiona chijha tichikhulupilila. Pakuti yani wakhulupilila chijha wachiona? 25 Ngati tichikhulupila icho tilibe, chimwecho sitichilindile kwa kuchilimbila mtima.