Kuchocha kwa mtima wabwino
1 Abale, nifuna mjhiwe nghani za ubwino wa Mnungu uwo apachidwa magulu ya wandhu amkhulupilila Kilisito aku Makedonia. 2 Okhulupila akumeneko adaesedwa kupunda ni kuvutika, nambho kukondwela kwao kudali kwa kukulu, amathangatila kupunda, ingakhale adali osauka kupunda. 3 Zenedi nikukambilani kuti adali othangatila kuchokana ni umo amakhozela ni kupitilila umo amakhozela. Palibe mundhu uyo wadakambila nambho adachocha kwa kufuna achinawene, 4 adatipembha kupunda kuti tichite njhito nawo yakwathangatila wandhu a Mnungu akujhiko la ku Yelusalemu. 5 Adachita njhito kupitilila umo timaganizila! Adajhichocha achinawene kwa Ambuye, ndiipo adajhichochanjho achinawene kwa ife, ngati Mnungu umo wamafunila.