Pular para o conteúdo
Publicidade

Vichito 5:1-4

NTNYBL2025 Nyanja

Ananiya ni Safila atonyenga

1 Kudali mundhu uyo wamatanidwa Ananiya pamojhi ni mkazake uyo watanidwa Safila adagulicha munda wao uwo adalinao. 2 Nambho Ananiya ni mkazake adagwilizana kubisa ndalama yakumojhi, ni kupeleka ndalama izo zidakhalila kwa atumwi. 3 Petulo wadaakambila, "Ananiya, ndande yanji wamulola Satana wakulamulile ni kukuchita umunyenge Mzimu Woyela kwa kubisa ndalama zakumojhi ya izo udagulicha munda? 4 Yapo udali ukali osaghuliche munda udali wako, niyapo udaghulicha ndalama zidalinjho zako ni udakakhoza kutumila ngati umo ufunila iwe. Ndande yanji udaganiza kuchita chimwechi mumtima mwako? Siudamnyenge mundhu, nambho wamnyenga Mnungu."

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    1 Koma munthu wina dzina lake Hananiya, pamodzi ndi mkazi wake Safira, anagulitsanso munda wawo. 2 Mogwirizana ndi mkazi wakeyo anapatulapo pa ndalamazo nazisunga, ndipo anatenga zotsalazo ndi kukapereka kwa atumwi.

    3 Koma Petro anamufunsa kuti, "Hananiya, chifukwa chiyani Satana anadzaza chotere mu mtima wako kuti unamize Mzimu Woyera ndipo wapatula ndi kusunga ndalama? 4 Kodi sunali wako usanagulitse? Ndipo utagulitsa ndalamazo sizinali mʼmanja mwako kodi? Nʼchiyani chinakuchititsa zimenezi? Iwe sunanamize anthu koma Mulungu."

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.