2 Simudaganizila ngati wandhu ajhiko lino umo aganizila, nambho Mnungu siwakung’anamuleni maganizo yanu kwa kuganizila bwino. Pamenepo ndipo simkhoze kujhiwa icho wafuna Mnungu ni kujhiwa chindhu chili cha bwino, ilo limkwadilicha ni kuchita ngati umo ifunikila.
Publicidade