Pular para o conteúdo
Publicidade

Romanos 16

Moni kwa wandhu osiyana siyana

1 Nikonda kumjhiwicha kwanu mlongo wathu Foibe, uyo wali mtumiki pa gulu la wandhu amkhulupilila Yesu ku Kenikelea. 2 Nikupembhani mlandileni bwino ndande waakhupilila Ambuye ngati umo ifunikila kwaalandila wandhu a Mnungu, mpacheni chalichonjhe icho siwachifune, pakuti iye wakhala wabwino kupunda kwa wandhu ambili ni kwaine.

Veja também