Poolo wamalizila maagizo
17 Nikupembhani achabale wanga mkhale maso ni anyiwajha apeleka kupatukana ni kwachita wandhu wina asiye chikhulupililo, ni anyiyawo achucha mayaluzo yayo mdayaluzidwa mkakhale patali nawo.