Pular para o conteúdo
Publicidade

Aloma 4

18 Ibulahimu pajha wadakambidwa mawu yajha yadali yolimba kuyakhulupila, nambho Ibulahimu wadaendekela kukhulupilila kuti Mnugnu siwamchite kukhala tate wa wandhu a maiko yambili, ngati umo yalembedwa mmalembo, "Mibadwa yako siikhale yambili ngati ndhondwa!"

Veja também