Pular para o conteúdo
Publicidade

Romanos 5

3 Osati yameneyope nambho tikondwela mavuto uku ni tijhiwa kuti mavuto yapeleka kulimba mtima pa kumkhulupilila Yesu, 4 ni kulimba mtima pa kumkhulupilila Yesu kupeleka kuchimikiza kwa mtima ni kuchimikiza kwa mtima kupeleka kukhulupilila. 5 Chikhulupi chimenecho sichitiphecha mtima, ndande Mnungu wathothila chikondi chake mmitima mwathu kwa njila ya mzimu woyela iyo wadatipacha.

Veja também