Pular para o conteúdo
Publicidade

1 Akolinso 1:1-3

NTNYBL2025 Nyanja

1 Ine Poolo, uyonatanidwa ni Mnungu kukhala mtumwi wa Kilisito Yesu ngati Mnungu wafunila, nili pano ni mbale Sositene.

2 Kwa gulu la wandhu amkhulupilila Yesu ilo lali ku Kolinso, anyiimwe mwachitidwa kukhala wandhu a Mnungu, ndande mwalunjana ni Kilisito Yesu, mudatanidwa kukhala wandhu a Mnungu pamojhi ni onjhe kila pamalo paliponjhe waapembha Ambuye wathu Yesu Kilisito, Mbuye wao, ni Mbuye wathu.

3 Nikupembhelani Ubwino ni mtendele kuchoka kwa Mnungu Tate wathu ni Mbuye wathu Yesu Kilisito.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    1 Paulo, woyitanidwa mwachifuniro cha Mulungu kuti akhale mtumwi wa Khristu Yesu ndi mʼbale wathu Sositene.

    2 Kupita ku mpingo wa Mulungu ku Korinto, kwa oyeretsedwa mwa Khristu Yesu ndi oyitanidwa kukhala opatulika ndiponso kwa onse amene amapemphera mʼdzina la Ambuye athu Yesu Khristu mʼdziko lonse lapansi, amene ndi Ambuye wawo ndi wathunso.

    3 Landirani chisomo ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate athu ndi Ambuye athu Yesu Khristu.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.