Pular para o conteúdo
Publicidade

1 Akolinso 12:4,7,12,22

NTNYBL2025 Nyanja

4 Pali mbhaso zosianasiana za Mzimu wa Mnungu, nambho zonjhe zichoka kwa Mzimu ni mweyujha mmojhi. 7 Nambho, mbhaso za muuzimu apachidwa wandhu osiyanasiyana dala za thangatile wandhu wina.

Thupi limojhi viwalo vambili

12 Ngati umo ili thupi ni limojhi, nambho lili ni viwalo vambili, atangati viwalo valivambili vichita thupi limojhi, nde umo ili kwa Kilisito.

22 Nambho pamalo pake, vijha viwalo va thupi ivovioneka vofooka ndeivo vifunika kupunda,

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    4 Pali mphatso zosiyanasiyana, koma Mzimu yemweyo.

    7 Tsono Mzimu amapereka mphatso kwa aliyense kuti ipindulire onse.

    12 Thupi ndi limodzi, ngakhale kuti lapangidwa ndi ziwalo zambiri. Ndipo ngakhale ziwalo zake zonse ndi zambiri, zimapanga thupi limodzi. Momwemonso ndi mmene alili Khristu.

    22 Mʼmalo mwake, ziwalo zathupi zimene zimaoneka ngati zofowoka ndizo zili zofunikira kwambiri,

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.