Pular para o conteúdo
Publicidade

1 Akolinso 3:15-17

NTNYBL2025 Nyanja

15 Nambho ngati njhito ya mundhu siiyomwe pamoto, siwapata mbhaso, nambho iye mwene siwalamichidwe ngati mujha wachelembuka pa moto.

16 Zene mjhiwa kuti anyimwe ni nyumba ya Mnungu ni kuti Mzimu wa Mnungu ukhala mkati mwanu? 17 Mnungu siwamuwanange waliyonjhe uyo wawananga nyumba ya Mnungu, pakuti nyumba ya Mnungu ni yoyela kupunda, ni nyumba imeneyo nimwachina wene.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    15 Ndipo ngati zidzanyeke ndi moto, sadzalandira mphotho koma iye mwini adzapulumukabe, koma monga ngati munthu amene wapulumuka mʼmoto.

    16 Kodi inu simukudziwa kuti ndinu Nyumba ya Mulungu ndipo kuti Mzimu wa Mulungu amakhala mwa inu? 17 Ngati wina aliyense awononga Nyumba ya Mulunguyo, Mulungu nayenso adzamuwononga ameneyo; popeza Nyumba ya Mulungu ndi yopatulika ndipo Nyumbayo ndi inu amene.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.