10 Mate yake mundhu wali ni chikhulupi chaching’ono wakakuona iwe, "Uli ni chikhulupi chachikulu," ukudya chakudya ivo vachochedwa mahokha, ichimikiza ata iye nayo wadye vindhu va mahoka? 11 Ni uyu mundhu wali ni chikhulupi cha ching’ono, uyo Kilisito wadamwalila ndande yake, wayomwechedwa ndande ya "kujhiwa kwako!" 12 Chimwecho, yapo mchita machimo kwa achabale wanu kwa njila iyi ni kwaika chilonda, mumlakwila Kilisito. 13 Chimwecho, ngati chakudya chikamkwiicha mbale wakhulupila wachite machimo, sinidyanjho nyama, dala sidamchita wakhulupila wachite machimo.
Publicidade
1 Akolinso 8:10-13
NTNYBL2025 Nyanja
Em outras traduções
- TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo
10 Pakuti ngati aliyense wachikumbumtima chofowoka akakuonani achidziwitsonu mukudya mʼnyumba yopembedzera mafano, kodi iyeyo sichidzamulimbitsa mtima kuti azidya chakudya choperekedwa nsembe kwa mafano? 11 Kotero kuti chifukwa cha chidziwitso chanu mʼbale wofowokayu amene chifukwa cha iye, Khristu anafa, wawonongeka chifukwa cha chidziwitso chanu. 12 Mukamachimwira abale anu motere ndikuwawonongera chikumbumtima chawo chofowokacho, mukuchimwira Khristu. 13 Nʼchifukwa chake ngati zimene ine ndimadya zichititsa mʼbale wanga kugwa mu tchimo, sindidzadyanso chakudyacho kuti mʼbaleyo ndisamuchimwitse.
Direitos das traduções citadas
Estes versículos te tocaram? Ore agora!
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.