18 Chimwecho, ife yao nghope zathu sizidavinikilidwe, tiuona ulemelelo wa Ambuye, ngati mukiyoo. Njhito ya Mzimu wa Ambuye iting’anamucha ife tilingane kupunda ni chifani chake kuchoka ulemelelo mbaka ulemelelo waukulu kupunda.