Pular para o conteúdo
Publicidade

Vichito 16

14 Mmojhi wa anyiwajha adativechela wadali Lidiya uyo wadachokela ku Tiyatila, uyo wamagulicha njhalu za mtengo wa ukulu. Iye wadali mundhu wa bwino. Ambuye Mnungu adamchita Lidiya wakhulupilile chijha wamakamba Poolo. 15 Iye pamojhi ni wandhu wonjhe yawo amakhala mnyumba mwake adabatizidwa. Ndiipo wadatitana kunyumba kwake, niwakamba, "Ngati muuona kuti ine nakhulupilila Ambuye Yesu, majhani kukhomo kwanga mkhale." Wadatipembha kupunda tipite kukhomo lake.

Veja também