Pular para o conteúdo
Publicidade

Maluko 10:13-16

NTNYBL2025 Nyanja

Yesu wapacha mwawi wana waang’onoang’ono

13 Wandhu wina adampelekela Yesu wana wang’onoang’ono waikile manja kuti wapache mwawi, nambho oyaluzidwa wake adaakaniza. 14 Yesu yapo wadaona chimwecho, wadakwiya ni kwaakambila, "Asiyeni wana waang’onoang’ono ajhe kwanga, ni simdachelekeza, ndande wandhu ali ngati wana anyiiawa nde sialowe muufumu wa Mnungu. 15 Zenedi nikukambilani, mundhu waliyonjhe uyo siwaulandila Ufumu wa Mnungu ngati wana wang’onoang’ono umo aulandilila, siwalowelatu muufumu wa Mnungu." 16 Ndiipo wadakhumbatila wana achameneo, ni kwaikila manja, ni kwaapacha mwawi.

Luka 18:18-30

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    13 Anthu anabweretsa ana kwa Yesu kuti awadalitse, koma ophunzira anawadzudzula. 14 Pamene Yesu anaona zimenezi anayipidwa. Anati kwa iwo, "Lolani ana abwere kwa Ine, ndipo musawaletse, pakuti Ufumu wa Mulungu uli wa onga awa. 15 Ndikukuwuzani choonadi, aliyense amene sadzalandira Ufumu wa Mulungu ngati kamwana sadzalowamo." 16 Ndipo ananyamula ana mʼmanja ake, ndi kuyika manja ake pa iwo nawadalitsa.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.