Pular para o conteúdo
Publicidade

Maluko 12:42-44

NTNYBL2025 Nyanja

42 Pamenepo wadajha maye mmojhi wafedwa ni mmunake uyo wadali wosauka, wadachocha senti ziwili. 43 Yesu wadaatana oyaluzidwa wake, ni kwaakambila, "Zenedi nikukambilani, maye uyu wosauka wachocha zambili kupitilila onjhe. 44 Wandhu wonjhe achocha ivo vakhalila pachuma chao, nambho maye uyu wafedwa ni mmunake pamojhi ni kusauka kwake wachocha vonjhe walinavo."

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    42 Koma mkazi wamasiye, wosauka anabwera ndi kuyikamo tindalama tiwiri ta kopala, tongokwanira theka la ndalama.

    43 Yesu anayitana ophunzira ake nati, "Zoonadi, ndikuwuzani kuti mayi wosauka wamasiyeyu waponya zambiri mʼthumbali kuposa ena onsewa. 44 Iwo apereka molingana ndi chuma chawo; koma iye, mwaumphawi wake, wapereka zonse anali nazo ngakhale zoti akanagulira chakudya."

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.