Pular para o conteúdo
Publicidade

Maluko 14:12,26,32,43,46

NTNYBL2025 Nyanja

Yesu wakudya chakudya cha Pasaka ni oyaluzidwa wake

12 Pa siku loyamba la pwando la mabumunda yayo yalibe amila, ni siku la kumpha mwana wambelele wa Pasaka, oyaluzidwa wake adamfunjha, "Bwanji, ufuna tipite kuti tikukonjele pwando la Pasaka?"

26 Ndiipo adaimba nyimbo ya kumtamanda Mnungu yapo adamaliza kuimba, adachoka ni kupita ku phili la Mizeituni.

Matayo 26:31-35; Luka 22:31-34; Yohana 13:36-38

Yesu wapembhela mbusitani ya Getisemane

32 Adafika pamalo yapo pamatanidwa Getisemane. Yesu wadaakambila oyaluzidwa wake, "Khalani yapa ine yapo nipita kupembhela."

Yesu wagwilidwa

43 Yesu yapo wadali wakali kukamba, Yuda mmojhi wa anyiwajha oyaluzidwa khumi ni awili, wadafika. Wadajha pamojhi ni gulu la wandhu anyiawo adali ni maupanga ni vibonga. Adatumidwa ni wakulu wa ajhukulu ni oyaluza athauko ni achogoleli.

46 Ndiipo, wandhu wajha adamgwila Yesu ni kumuika panjhi pa ulonda.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    12 Pa tsiku loyamba la Phwando la Buledi wopanda yisiti, nthawi imene mwa mwambo inali ya kupha mwana wankhosa wa Paska, ophunzira a Yesu anafunsa Iye kuti, "Mufuna tipite kuti kumene tikakonzekere kuti mukadyere Paska?"

    26 Atayimba nyimbo, anapita ku phiri la Olivi.

    32 Ndipo anapita ku malo otchedwa Getsemani, ndipo Yesu anati kwa ophunzira ake, "Khalani pano pamene Ine ndi kupemphera."

    43 Iye akuyankhulabe, Yudasi, mmodzi mwa khumi ndi awiriwo, anatulukira. Anali ndi gulu la anthu litanyamula malupanga ndi zibonga, otumidwa ndi akulu a ansembe, aphunzitsi amalamulo, ndi akuluakulu.

    46 Anthu anamugwira Yesu ndi kumumanga.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.