Pular para o conteúdo
Publicidade

Maluko 14:61-64

NTNYBL2025 Nyanja

61 Nambho Yesu wadakhala chete, siwadakambe kandhu. Mjhukulu wamkulu wadamfunjhanjho, "Bwanji iwe nde Kilisito, Mwana wa Mnungu uyo watamandidwa?" 62 Yesu wadamuyangha, "Nde ine. Ni anyiimwe simumuone ine mwana wa Mundhu nakhala janja la kwene la Mnungu wambhavu, ninijha mmitambo ya kumwamba." 63 Mjhukulu wamkulu wadang’amba njhalu zake kulangiza mbwayi ni kukamba, "Bwanji, tifunanjho amboni a chiyani? 64 Mwachinawene mwavela umo wamkafulila Mnungu" Anyiimwe muona bwanji? Bwalo lonjhe lidamlamula waphedwe.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    61 Koma Yesu anakhala chete ndipo sanayankhe.

    Mkulu wa ansembe anabwereza kumufunsa Iye kuti, "Kodi ndiwe Khristu Mwana wa Wodalitsikayo?"

    62 Yesu anati, "Ndine, ndipo mudzaona Mwana wa Munthu atakhala kudzanja lamanja la Wamphamvuzonse ndipo akubwera mʼmitambo ya kumwamba."

    63 Mkulu wa ansembe anangʼamba zovala zaunsembe zake. Iye anafunsa kuti, "Chifukwa chiyani tikufuna mboni zinanso? 64 Mwamva mwanowo. Muganiza chiyani?"

    Onse anavomereza kuti ndi woyenera imfa.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.