Pular para o conteúdo
Publicidade

Maluko 15:42-46

NTNYBL2025 Nyanja

Yesu wazikidwa

42 Ujhulo yapo udawandikila. Pakuti lidali Siku lo konjekela kupumulila, 43 wadajha Yusufu uyo wamachokela ku mujhi wa Alimasaya, mundhu wa bwalo la milandu, wamalemekezeka kupunda wadafika. Mundhu mmeneyo wamalindililila kujha kwa Ufumu wa Mnungu. Chimwecho Yusufu wadampitila Pilato popande kumuopa, wadampembha wampache thupi la Yesu. 44 Pilato wadazizwa yapo wadavela kuti Yesu tayali wathomwalila. Ndiipo, wadamtana wamkulu wa asikali ni kumfunjha ngati Yesu wathomwalila. 45 Pilato yapo wadakambidwa ni yujha wamkulu wa asikali kuti Yesu wathomwalila, wadamvomeleza Yusufu walitenge thupi la Yesu. 46 Yusufu wadaghula sanda, wadalichicha panjhi thupi la Yesu, wadalivilingila sanda. Adaliika pambhanga iyo idakumbidwa pa mwala wolimba. Ndiipo wadaugunghulicha mwala pakhomo pa ijha mbhanga.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    42 Linali Tsiku Lokonzekera (kunena kuti, tsiku lomwe limatsatizana ndi Sabata). Choncho madzulo atayandikira, 43 Yosefe wa ku Arimateyu, mkulu wolamulira odziwika bwino, amene amadikirira ufumu wa Mulungu, anapita kwa Pilato molimba mtima ndi kukapempha mtembo wa Yesu. 44 Pilato anadabwa pakumva kuti anali atamwalira kale. Anayitana Kenturiyo, namufunsa ngati Yesu anali atamwalira kale. 45 Atawuzidwa ndi Kenturiyo kuti zinali motero, anapereka mtembowo kwa Yosefe. 46 Choncho Yosefe anagula nsalu yabafuta, natsitsa thupi, ndipo analikulunga mʼnsalu, naliyika mʼmanda amene anawagoba pa mwala. Kenaka anagubuduza mwala umene anatseka nawo mandawo.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.