Yesu watengedwa kupita kumwamba
19 Ambuye Yesu yapo adamaliza kukamba ni oyaluzidwa wawo, adatengedwa kupita kumwamba, adakhala kubendeka la kwene la Mnungu.