Mbhavu ya uthenga wa bwino
16 Ine siniona njhoni kuuzila uthenga wa Bwino, wene ni mbhavu ya Mnungu, iyo yaombola wandhu wonjhe amkhulupilila Yesu. Kuyambila Ayahudi ni anyiawo osati ayahudi. 17 Pakuti uthenga wa bwino walangiza umo Mnungu wafunila tikhale kuti tivomelezeke pachogolo pake, chindhu ichi chichitika kwa kumkhulupilila Yesu Kilisito, palibe china kupitilila chimecho, ngati umo yalembedwa mmalembo, "Mundhu wovomelezeka kwa Mnungu siwakhale kwa kumkhulupilila Mnungu."