14 Chipano sampembhe bwanji iye samkhulupilila? Nianyiiwo, samkhulupilile bwanji ngati sadavela nghani zake? Nisavele bwanji ngati palibe mundhu olalikila? 15 Ni wandhu salalikile bwanji ngati sadapelekedwe? Ngati umo yalembedwa mmalembo ya Mnungu, "Chindhu chokwada kupunda kujha kwa wajha alalikila Uthenga Wabwino!"
Publicidade