10 Ndande yanji iwe umlamula mbale wako? Iwe ndande yanji umdelela mbale wako? Ife taonjhe sitiime pachogholo pa mpando wa chifumu wa Mnungu. 11 Pakuti yalembedwa mmalembo ya Mnungu kuti,
"Ngati umo nikhalila Ambuye akamba,
Kila mundhu siwanigwadile,
kila mmojhi siwakambe mwene kuti ine ni Mnungu"
12 Chipano kila mmojhi wathu siwakambe nghani zake mwene pachogholo pa Mnungu.